Emmanuel Chisawa

Emmanuel Chisawa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Emmanuel Chisawa, Eastern Cape, Blantyre.

30/08/2026

DEPUTY MINISTER NORMAN CHISALE DONATES 200 BAGS OF CEMENT AND K5 MILLION TO MZIMBA CCAP CHURCH

Dalitso Singano Kabambe kosaka mavoti 2025. Voti osamayiphweketsa.
30/08/2026

Dalitso Singano Kabambe kosaka mavoti 2025. Voti osamayiphweketsa.

Katswiri wa maphunziro a chisilamu mdziko lino Grand m***i Muhammad Uthman wapempha boma kuti likhazikitse lamuro lofuna...
30/08/2026

Katswiri wa maphunziro a chisilamu mdziko lino Grand m***i Muhammad Uthman wapempha boma kuti likhazikitse lamuro lofuna kutetedza amayi pa nkhani yokhuzana ndikuyeza umwini wa ana (DNA partenity test).

Katswiriyu wati aliyense oyeza umwini wa ana ndipo zosatira zikatuluka kuti mwanayo Ali wake akuyenera azimangidwa ndikugwira ndende. Iye wati izi ziteteza nkhaza zomwe amayi azikumana nazo m'mabanja.

"Mulungu salora kukayikira wa chikondi wako kopanda umboni ogwirika.....kuyezetsa umwini ndi chizindikiro chokayikira wa chikondi zomwe ndizoletssedwa... aliyense ochitira nkhaza amayi alangidwe... zotsatira zikatuluka kuti mwana ndi wako ukuyenera kulandira chilango"

Iwo alankhura kusatira kafukufuku yemwe watutumutsa Amalawi ochuluka omwe waonetsa kuti abambo asanu ndi atatu pa abambo khumi akulera ana omwe sali obara Iwo eni. Izi zapangitsa kuti Amalawi ochuluka akhamukire ku Malo oyeza umwini wa mwana.

30/08/2026

Asalam alaikum warahmatullah wabarakatuh

Nkhani yake ikuterotu kumva ulaliki kumeneko

Mufuti Chibekete akutero

Lero ndili mwa

30/08/2026

Uyu watiwonjedza koma

30/08/2026

Izi lero ayi tipume Kaye

30/08/2026

Lero tikupanga za yawe Kaye

30/08/2026

Kumapemphera kumeneko not always online busy miseche.

Mwalowera kuti lero ife tili uku

29/08/2026

Eish 🙌

Address

Eastern Cape
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Emmanuel Chisawa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share