2025 APM MY VOTE

2025 APM MY VOTE The right to change the life of Malawians

Zonse chifukwa chosawa ulamuliro wabwino😭💔Oyendetsa galimoto ena komanso achibale a dalaiva yemwe zikumveka kuti waombel...
22/09/2024

Zonse chifukwa chosawa ulamuliro wabwino😭💔

Oyendetsa galimoto ena komanso achibale a dalaiva yemwe zikumveka kuti waombeledwa ndi apolisi pa road block ya 4 miles ku Zomba ayamba kusonkhana ku polisi ya Zomba.

Titafika pamalopa tapeza achibale a malemuwa akulira pa polisiyi ndipo oyendetsa galimoto ataima pa polisiyi.

Ena mwa omwe anali nawo mgalimotoyi padakali pano akuwalemba ma statement.

Wolemba Tiyese Monjeza.

Copied (times 360 Malawi)

21/09/2024

Arthur Peter Mutharika vote yathu

Inu tikutitu 2025 APM MY VOTE   with Madam first lady kuvala zoziwa🔥✨Don't forget to follow for more information
21/09/2024

Inu tikutitu 2025 APM MY VOTE with Madam first lady kuvala zoziwa🔥✨

Don't forget to follow for more information

Zosatira za mitsonkhano ya DPP ndi MCP zayamba kufika kuno Omwe akuonera ntsonkhano wa DPP pa times ndi 4.1K Pomwe  akuo...
21/09/2024

Zosatira za mitsonkhano ya DPP ndi MCP zayamba kufika kuno

Omwe akuonera ntsonkhano wa DPP pa times ndi 4.1K

Pomwe akuonera wa MCP pa times ndi 947

Kkkkkkkk boma layamba kuoneka lokha

Happening now in NorthDon't forget to follow 2025 APM MY VOTE  for more information...🔥🔥 Akumva pain wina
21/09/2024

Happening now in North

Don't forget to follow 2025 APM MY VOTE for more information...🔥🔥 Akumva pain wina

21/09/2024
21/09/2024

Welcome to 2025 2025 APM MY VOTE ✅

Address

Post Office Box 256 Blantyre
Blantyre
556688

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when 2025 APM MY VOTE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share