Kairos Global Initiative

Kairos Global Initiative A mission-driven enterprise empowering youth and women with skills, serving clients with excellence, and building lasting impact. Join the journey.

Kairos is where transformation begins. Be the change.

Amangwetu, Pokondwelera intake ya September, tigaweko ya lunch yapa chiwaya kwa anthu angapo. Comment and tag atleast an...
04/09/2026

Amangwetu, Pokondwelera intake ya September, tigaweko ya lunch yapa chiwaya kwa anthu angapo. Comment and tag atleast anthu 5 pa post imeneyi. Tisankha randomly.

Amangwetu, komabe mwadzuka bwino mmesa?
04/09/2026

Amangwetu, komabe mwadzuka bwino mmesa?

Amangwetu kumaonatu yolowela  mwezi watha kumene UWU πŸ˜‚ πŸ˜‚
03/09/2026

Amangwetu kumaonatu yolowela mwezi watha kumene UWU πŸ˜‚ πŸ˜‚

MWADZUKA KAPENA MWASWERA? TAPANGENI TAG AMNZANU AJA ADZIWE. NKHANI YABWINO KWA NONSE OMWE MUMAYEMBEKEZELA KUPHUNZILA NTC...
03/09/2026

MWADZUKA KAPENA MWASWERA? TAPANGENI TAG AMNZANU AJA ADZIWE. NKHANI YABWINO KWA NONSE OMWE MUMAYEMBEKEZELA KUPHUNZILA NTCHITO YA MANJA KU KAIROS, SCHOOL YOKHAYO YOMWE ILI NDI MALO, AKATSWILI ODZIWA KUPHUNZITSA KOMANSO ZIPANGIZO ZOYENELERA.

SEPTEMBER INTAKE YATSEGULIDWA NDIPO M***A KULMBETSA, MNDANDANDA WA MAPHUNZIRO ULI MOTELE:

1. ELECTRICAL INSTALLATION & REPAIR OF HOME GADGETS
(ZAMAGETSI) FEES: k129,000 YOKHA

2. ICT & COMPUTER SKILLS (LUSO LA COMPUTER)
FEES: k95,000 YOKHA

3. PHONE REPAIRING (UKADAULO OKONZA MA PHONE)
FEES: K129,000 YOKHA

MAPHUNZILOWA AMACHITIKILA KU KAIROS TRAINING CENTER KU LIMBE MU MZINDA WA BLANTYRE NDIPO KWA ANTHU AKUTALI, MALO A SELF BOARDING ALIPO PA MTENGO WA K45,000 YOKHA.

REGISTRATION FEE: K10,000

LEMBETSANI LERO MALO ASANATHE PA NUMBER IYI: 0881 23 99 55

Amangwetu, September tu akuyenda chonchi, tag omwe akumanga nyumba tathandize mwaulele mwezi Uno project isunthe.
01/09/2026

Amangwetu, September tu akuyenda chonchi, tag omwe akumanga nyumba tathandize mwaulele mwezi Uno project isunthe.

Partner Kairos Global Initiative walowa September ndi πŸ”₯πŸ”₯ Blantyre Maxsherrians mukuti bwanji apa?

"Mu September tufuna kuthandiza anthu awili omwe akumanga nyumba and afika pa level ya wiring ya magetsi.

Tiwapangile wiring mwaulele, starting from site survey, discussing quantities zofunikila zonse and kuwapelekezanso ma shop a mitengo yabwino.

Koma ntchito yonse ya wiring will be done for free.

We only have 2 slots, those interested reach out to us on 0881239955.

Location ikhale ku Blantyre kuno and surrounding areas"

01/09/2026

It's a new month! September To Remember! Tatchulani chimodzi chomwe mukufuna mutakwanilitsa mwezi Uno, Mulungu alipo inu, atha kukuchitilani.Dzukani tiyambep

Amangwetu, Kodi nanga aka Ka slim, Ka Sim card, 64GB akugulileni ndani? Mpangeni tag mwansanga mumuuze kuti nanunso zabw...
31/08/2026

Amangwetu, Kodi nanga aka Ka slim, Ka Sim card, 64GB akugulileni ndani? Mpangeni tag mwansanga mumuuze kuti nanunso zabwino mumazifuna, mmawali Katha kukhala Kali mmanja mwanu

Amangwetu tsiku linali bwanji?
31/08/2026

Amangwetu tsiku linali bwanji?

31/08/2026

Amangwetu, Lunch yanu koma ikuyenda bwanji? Nenani moopa ndani? We drop some good news masanawu.

31/08/2026

Ambiri akudalira inuyo, kwanu kuja osintha zinthu ndinuyo, kugiva is not an option. Ambuye akupatseni mphamvu ndi chisomo choimabe kuti mukwanilitse. Mwadzuka?

Address

Limbe
Blantyre
265

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kairos Global Initiative posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category