Whom A'm I Before God?

  • Home
  • Whom A'm I Before God?

Whom A'm I Before God? Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Whom A'm I Before God?, Library, .

10/04/2024
31/07/2021

Morning people of God? Cheating does not pay , cheating can lead you to death both physically and spiritually, 👄

Masalimo 119:11 Ndinawabisa mau anu mumtima mwanga k*t ndisalakwile inu. Ambili mumtima mwathu ndinkhokwe imene tikusung...
16/11/2020

Masalimo 119:11 Ndinawabisa mau anu mumtima mwanga k*t ndisalakwile inu. Ambili mumtima mwathu ndinkhokwe imene tikusungamo machimo ochuluka koma tikuenera kusintha. Lapani machimo anu nthawi ilipo , koma Mulungu kadzati kwatha kainu kulibe kulapa.

24/02/2017

Zireken Namsongole ndi Tirigu zikulire pamodzi pak*t ikudza nthaw imene mwinimunda adzabwera ndipo zose adzadziwa koziika pak*t tirigu kwake ndkunkhokwe pomwe namsonge wakumoto basi, inu ndinu yani? pak*t ochita zoipa onse ndiw anamsongole pamene olandira yesu natirigu inu ndinu ayani?~ sankhan mbali lero pocomenta pamene tkudikra utheng wachilimbikitso

27/04/2016

Kkkkk Pali mitu iyi yankhan yomwe inu mukufunika mutasank kt ilembdwe anth asangalarep kmaso kuphuzirap 1:Tsokalienda 2:Wachikond osakhumudwtsa moyowanga 3:Chinamuluma chakuda "sankhan ndpo nkhan idzayamb kulembedw malinga ndkuchuluka kwaanth amen aivotela.

27/04/2016
18/04/2016

inu amen mumaph lifesklls can u traslate "stress and anxiety''.

Address


KASUNGU

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Whom A'm I Before God? posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your organization to be the top-listed Government Service?

Share