NRC

NRC A game changing political philosophy to transform Malawian masses.

25/11/2025

Join the NRC National Forum on Whatsapp.

Link in the Comment section.

Tomorrow bwana President akhala live a podcast malawi kuvukuta National Budget.  Komaso akhala ndi program yomwe akambep...
25/11/2025

Tomorrow bwana President akhala live a podcast malawi kuvukuta National Budget.

Komaso akhala ndi program yomwe akambepo nkhani za chuma. Tiyeni ku page yawo tikaikepo maganizo athu pa zomwe mungafune kumva.

https://www.facebook.com/share/1AHnC9Y6PF/

Tomorrow in the morning we will be shooting With Caswell Mkanda. We will discuss in depth on some economic issues. What would you like to hear in our conversation?

In the evening we will be live on podcast Malawi analysing the mid year budget statement that was presented by Honourable Mwanamvekha. What areas would you like to be tackled?

NRC muli magulu a anthu zigawo zonse. Comment the district you're in and mupatsidwa link la dela Lani.Like and share.
24/11/2025

NRC muli magulu a anthu zigawo zonse. Comment the district you're in and mupatsidwa link la dela Lani.

Like and share.

24/11/2025

Popanda chikondi utsogoleri sungakomele anthu wamba.


Recently takhala tikuona dvuto losowa kwa nyumba za rent. Izi zili choncho tili ndi Malawi Housing Corporation komaso ma...
23/11/2025

Recently takhala tikuona dvuto losowa kwa nyumba za rent.

Izi zili choncho tili ndi Malawi Housing Corporation komaso ma bungwe ena a boma amane amayang'anila ntchito zomangamanga. Kupatula apo tili ndi nyumba ma town a Lilongwe, Blantyre, mzuzu zomwe linamanga ndi boma la Kamuzu ndi Malo ena a boma ndi nzika za dziko lino.

Kodi chifukwa china boma silionetsa chidwi chomanga nyumba zamakono kuti nzika zisamasowe pokhala. Nanga bwanji mu budget yadzulo boma likupeleka mwayi kwa a Malawi othekela amene ali kunja kwa dziko lino kumanga nyumba zamakono ngakhale sanatambasule kuti nyumba zimenezi zipeleka mwayi kwa anthu wamba.

Ife ngati anthu wamba timangosilila tikapita dziko la eni mmene ma boma awo amakondela nzika zawo poonetsetsa kuti zili ndi Malo okhala a abwino. Ifeso ngati nzika ndi udindo wathu kufusa mafunso kwa adindo kuti atithandize. Ku dyeledwa ndalama ndi ma agent ngati sikukukwanani tiyeni tikhale tizisiye chonchi mpaka kale.

61 years of independence ma council athu akukanika ukugwila ntchito zake moyenela. Ndi chifukwa chani council imakanika ...
22/11/2025

61 years of independence ma council athu akukanika ukugwila ntchito zake moyenela.

Ndi chifukwa chani council imakanika kulemba a chitetezo ake monga kukhala ndi Lilongwe police department monga timaonela Lilongwe water board komaso Blantyre water board?

Kuchepa kwa chitetezo ma town zimabwezeletsa mbuyo ma business ndi ma services ena. Ndi zosayenela kuti ma council adzitenga anthu omwe sanapatsidwe upangili opeleka chitetezo mu council monga anyamata aja amathamangitsa ma vendor Malo osayenela.

Nduna ya kale ya local Government a Blessings Chisinga ananenapo kuti boma Lili ndi ma plan ofuna kuti ma council adzilemba a police awo koma nkhani imeneyo sinapitilile.

Ngati muli nzika yokonda ma dziko Lani tiyeni tiwafuse a Nduna a Local government kuti ife nzika tikufuna ma council akhale ndi Police department monga Lilongwe police department, Blantyre police department kuti adzilimbikitsa chitetezo chama town ndi ma district ena.

Timve maganizo anu komaso apangeni tag adindo kuti atithandize anthu wambafe.

Mandate ya ulamuliro omwe ulipo pano itha 2030. A Malawi tonse tikuyenera kukhala ndi chidwi ndi dziko lathu polangiza u...
15/11/2025

Mandate ya ulamuliro omwe ulipo pano itha 2030. A Malawi tonse tikuyenera kukhala ndi chidwi ndi dziko lathu polangiza utsogoleri kuti zaka zisanu zisapite padela.

Tiyeni titengelepo mwayi kutsatila zokambirana za ku nyumba ya malamulo ( *Parliament)* ndikufunsa adindo otiyimilira kuti abweletse ma bill okomera aMalawi. Akuyeneranso kuonetsetsa kuti ma policy omwe alipo ndi ena omwe abweretse akhale okomela TONSE.

Kusitha dziko kumadalira kupereka mafunso ku nthambi za boma monga Nyumba ya Malamulo pakuti ndi imene inapatsidwa mphamvu zositha malamulo.

Kodi ndi chifukwa chiyani ngati dziko tilibe kampani ya migodi imene imayenela kuti ikhale pa Malawi Stock Exchange kuti tonse monga mzika tikhale ndi mwayi okhala ndi umwini ku ma kampani onsewa a cement ndi quarry zomwe zimapezeka m'midzi?

Tikukamba izi chifukwa ife monga dziko sitikuyenera kupereka chuma chonse kwa anthu obwera.
Chuma chikuyenera kugawidwa moyenera kuti eni nthaka adzipindulanso mokwanira. Boma silikuyenera kukhala patsogolo kulolera kuti chuma chadziko chidzitengedwa ndikupindulira mayiko akunja komanso andale akatangale, omwe alibe chidwi chotukula miyoyo ya anthu, pomwe mzika zake zikukulukutika ndiumphawi.

Tiyeni tidzifunse ngati dziko kuti vuto ndi chiyani m'Malawi wamba, yemwe akusowa pogwira, kukhala ndi gawo muma kampani a miyala yamtengo wapatali?

Tiyeni tikhale ndi chidwi ndi chuma chathu chomwe Mulungu anatidalitsa nacho.

Wathu.
Yathu
Chathu

*TIKUFUNA KUMVA MAGANIZO ANU* Kodi kwa inuyo, *Prosperity* kapena kuti *Kutukuka* ngati dziko mumangofokoze motani monga...
13/11/2025

*TIKUFUNA KUMVA MAGANIZO ANU*

Kodi kwa inuyo, *Prosperity* kapena kuti *Kutukuka* ngati dziko mumangofokoze motani monga aMalawi.

Tikunenatu inu a Malawi omwe tinamenyeledwa ufulu kuyambila John Chilembwe, kubwela kwa Kamuzu mpaka pano tikunena kuti ndi dziko lotsata democracy.

Inuyo pa nkhani ya Prosperity kapena kuti Kutukuka ngati dziko mungakufotokezele bwanji?

n'kutani?
tili pati ngati dziko?
okhutira?
timakhumba titafika pati ngati dziko?

Timve maganizo anu!

Osaiwala kupanga follow our page.

Like and share the post.

🇲🇼 NRC on PROSPERITY: Building a People’s Economy for AllMalawi is rich in potential, yet our people remain poor. Every ...
12/11/2025

🇲🇼 NRC on PROSPERITY: Building a People’s Economy for All

Malawi is rich in potential, yet our people remain poor. Every day, ordinary Malawians wake up early, work hard, and hope for a better tomorrow, but our systems continue to fail them. NRC believes it’s time to change that story.

PROSPERITY is not just about money, it’s about dignity, fairness, and opportunity for every Malawian. It means creating an economy that works for the people, not just for a few at the top.

Under the banner of Prosperity, NRC envisions:
✅ A People’s Economy that supports local industries, farmers, and entrepreneurs.
✅ Job creation through innovation, technology, and small-scale enterprises.
✅ Fair trade and fair wages so that hard work truly pays.
✅ A corruption-free economy where national resources benefit all, not a few.
✅ Economic decentralization: empowering districts to plan and drive their own development.

We believe Malawi can rise again if we rebuild our economy from the grassroots up. We must invest in our people, our land, and our ideas, not wait for foreign aid to define our destiny.

“Prosperity is when every Malawian can afford a decent life, not just survive it.”

The future belongs to those who dare to think differently. NRC dares to imagine a Prosperous Malawi — for all, by all, and with all.


Address

Lilongwe

Telephone

+265995305382

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NRC posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share