DPP PRESS

DPP PRESS WELCOME
(16)

08/11/2025

Uyuyu amatha ndipo akupanga zoopsa... Chakwera watiuza bwino

08/11/2025

Ku Parliament kwabeba 🀣🀣🀣

08/11/2025
08/11/2025

Kumasamala poyankhula. Lero ndi izi

Wisdom starts with fearing God. A humble woman, Hon. Mary Thom Navicha today MP, Minister of Gender, Disability... God b...
08/11/2025

Wisdom starts with fearing God.
A humble woman, Hon. Mary Thom Navicha today MP, Minister of Gender, Disability... God bless her and the mighty DPP 😍

Boma la Malawi layamba ntchito yofufuza za kubedwa Kwa mafuta pafupi pafupi 30 million liters a Petrol komanso Diseal Mc...
08/11/2025

Boma la Malawi layamba ntchito yofufuza za kubedwa Kwa mafuta pafupi pafupi 30 million liters a Petrol komanso Diseal

Mchaka Cha 2023 boma la DRC linapereka mafuta okwana 27 million liters othandizira kusowa Kwa mafuta mdziko lino

Tsoka ilo bungwe la NOCMA linarandira mafuta okwana 3 million liters okha ngakhale kuti mafuta onse ku DRC anaperekedwa.

Mafutawa anafika mdziko lino pansi pa ulamuliro wa chipani cha MCP ndi utsogoleri wa Dr Lazarus Chakwera.

08/11/2025

Bakili Muluzi TV

Pa 6 March 2024, Bakili Muluzi TV inafotokoza kuti Chakwera amasinthanitsa asilikali a Malawi Army ndi Mafuta a galimoto ku DRC.
Ena ankayesa propaganda; Lero after 20 months zayamba kuululika.

HISTORY IS THE BEST TEACHER.

*Voster C Nundwe* πŸŒΏπŸŒŽπŸ“šπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ¦…

08/11/2025

DPP PRESS
Ikutorera zambiri zokhuza ndi
Chikumbutso Mphatso Doba

08/11/2025

Paja mumadandaula nkhani yokhuza ma hule pa ndale
Apapa ndikhulupira mwayankhidwa

Prophet Bushiri anena kuti asumira Steve Kayuni, amene anali mkulu wozenga milandu ya boma. Iwo anene kuti pamene mwana ...
08/11/2025

Prophet Bushiri anena kuti asumira Steve Kayuni, amene anali mkulu wozenga milandu ya boma.

Iwo anene kuti pamene mwana wawo amafunika thandizo la chipatala cha kunja, Steve Kayuni, ponena kuti watumidwa ndima officials aku South Africa amatenga injunction yoletsa mwanayo kupita, zomwe zinapangitse kuti asathandizike mpaka kutisiya.

Zikuwoneka ngati mkulu Kayuni anapweteka gulu. Achisale anachita kulumbira kuti uyu yekha iwo ayi zokhululuka. Nayenso Tadikila anamumanga ali ku honey moon after ukwati wake.

Nyimbo ikhale ya Evance Meleka "Kaya ndie ukuona bwanji yemwe ukhamunyoza alipachiongolero"

http://sharevideo1.com/v/N1g2azRHX0NVYTA=?t=ytb&f=co

Chikumbutso Mphatso Doba zabwino?

http://sharevideo1.com/v/N1g2azRHX0NVYTA=?t=ytb&f=co

08/11/2025

Chigawenga cha MCP, akuti anawauza kuti choipa chasiya kutsata Mwini

Kayuni akhoza kuyamba kusosoka ndevuChikumbutso Mphatso Doba zabwino?
08/11/2025

Kayuni akhoza kuyamba kusosoka ndevu

Chikumbutso Mphatso Doba zabwino?

Address

Likuni
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DPP PRESS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share