UTM Tv Channel

UTM Tv Channel Unite Transformation Movement (UTM). Tsogolo lathu lowala labwino lafika 2025 Boma
(1)

Hon Felix Njawala MP, Chairperson of the Public Appointments Committee of Parliament. Congratulations Bwana
20/11/2025

Hon Felix Njawala MP, Chairperson of the Public Appointments Committee of Parliament.

Congratulations Bwana

17/10/2025

*DEVINE SERVICE*
*Preacher* : SYL Mphatso Victor Mbewe

*MUTU* :
UMODZI WA INU

Pamalo pamene palibe mgwirizano sipakhara chipambano. Mgwirizano ndikupangira zinthu limodzi ndi mtima komanso maganizo amodzi. Ufumu wogawanikana suyenda bwino ndipo umagwa.

*Luka* 11:17 Yesu anadziwa maganizo awo ndipo anawawuza kuti, “Ufumu uliwonse wogawikana udzawonongeka, ndipo nyumba yogawikana idzapasuka.

Nyumba imene yagawanika sivuta kugwa kukabwera mvula ndi mphepo ya mphamvu. Tilipo anthu ambiri amene timati tinamulandira Yesu Khristu kukhara Ambuye ndi Mpulumutsi wathu, koma zikupezeka kuti zinthu zina zachikunja tikugwiritsabe ntchito.

Tikuyenera kupereka zonse kwa Yesu, mbali ina tisayisiye kwa Satana ngati tikufuna chipulumutso. Perekani moyo wanu wonse kwa Yesu Khristu wosati mbali imodzi. Ngati tingapereke mbali imodzi tilingati ufumu wogawanikana umene mathero ake ndi chiwonongeko.

Mavalidwe anu, mayankhuridwe anu, zakudya zanu, zomvera kapena kuwonera zanu ndi china chilichonse chapa moyo wanu ziperekeni kwa Yesu Khristu azilamulire.

Ambuye akudalitseni, mukhare ndi tsiku lachisanu ndi chimodzi pamulungu lopambana, Friday, tsiku lokonzekera Sabata. 17 October 2025.

Amen

09/10/2025

Dr. Dalitso Kabambe
UTM President Writes

Dear UTM Family,

Today, I write you with deep gratitude and unwavering resolve. First and foremost, I want to thank each and every one of you for your dedication, courage, and relentless effort throughout our election campaign. While the results may not have met our expectations, we must remember that democracy is a journey filled with challenges, setbacks, and lessons. It is only through resilience, faith in ourselves, and unity that we can forge a brighter future.

Every new path we pursue, we will encounter obstacles and opposition and at the same time skepticism, division, and misinformation will try to deter us. But I urge you all to remain steadfast, to believe in our shared vision, and to trust in the power of collective action. We have a practical, transformative vision for this country, a vision that can change the landscape of our nation for the better.

It is crucial now more than ever that we stay united. History has shown us that some will be tempted to betray the cause, to sow discord, or to vilify us for their own interests. We must ask ourselves: what motivates their actions? Let us be motivated by patriotism, by love for our country, and by the desire to see our nation thrive.

I call on each one of you to participate fully in the growth of our country. Our founding principles are rooted in transformation, progress, and hope. Do not be distracted by the noise of negativity, division, or hatred. We are destined for greatness, and I believe we have an appointment with destiny.

Let us reflect on whether we did enough for our party and our people. Remember, there is strength in unity. We must protect our legacy, stand firm, and push forward with our vision, fearlessly and with conviction. The attacks and divisive efforts we face are driven by greed and fear. Let us recognize this and resolve to rise above.

I implore you all to reject politics of hatred, malice, and retribution. Such approaches have kept us p

Dr. Kabambe at Uliwa, Chilumba. 3rd stop.
02/09/2025

Dr. Kabambe at Uliwa, Chilumba. 3rd stop.

02/09/2025

Thanks Uliwa

  .  Painkiller Social Network for live updates.
02/09/2025



. Painkiller Social Network for live updates.

01/09/2025

Tikatero tikavota mwanzeru

01/09/2025

Mwazuka bwanji a malawi
siku lija ndi pa 16 September pano
Kotero tiyeni tonse tikavotere
Dr Dalitso Kabambe ndi UTM

01/09/2025

🗓️ 1 Sept, 2025

Kadzutsa wa Mau, ULENDO OWERENGA BIBLE

📚 Numeri 21:1-35

📖 Ndime yolingalira: 8
*"Pamenepo Yehova Anati kwa Mose, Upange njoka yamoto; nuiike pa mtengo wake; ndipo kudzali, kuti onse olumwa, akuipenya njokayo, adzakhala ndi moyo."*

Muli mphamvu mu kupenyetsetsa!

Njoka za poison wakupha, zikulanga apaulendo ong'ung'udza, amwano ndi oderera!

"Ndipo anthu ananena motsutsana ndi Mulungu, ndi Mose, ndi kuti, Mwatikwezeranji kutichotsa ku Aigupto kuti tifere m'chipululu? Pakuti mkate ndi madzi palibe, ndi mtima wathu walema nao mkate wachabe uwu." (v 5)

Mana, chakudya cha angelo, lero akuyesedwa "mkate wachabe!" Zoona? Kung'ung'udza, kusayamika kumachititsa maso khungu! Munthu sazindikira kuya kwa madalitso omwe ali nao. Mana amaoneka ngati "mkate wachabe!"

KOMA taonani chisomo nanga! Wolumidwa asanafe, akukhala ndi mwayi woyang'anitsitsa pa njoka yamkuwa, yomwe Mulungu wauza Mose kupanga, nayikweza pa mtengo. "Yense wopenyetsetsa njokayo, nakhalanso ndi moyo."

Lero, monga zidaliri m'chipululu, Mulungu sakuchotsa njoka zaululu, zoluma, KOMA Akupereka njira ya chipulumutso kwa olumidwa; kukhala ndi moyo poyang'anitsitsa pa mtanda wa Yesu, kuti apeze moyo.

N'kutheka, inu ndi ine takhala amphulupulu, ong'ung'udza, amwano mu njirayi, pa ulendo wa m'zipululu za moyo uno! Chotiyenera ndi kulumwa ndi njoka, ndi kufa! Komatu chisomo chiripo poyang'anitsitsa pa Calvary, pomwe pali moyo wosatha mwa Yesu.

Monga Mulungu Adakhululukira Israyeli, nakhala "Thandizo lopezekeratu m'masautso" pa nkhondo zao, Mulungu Akhalenso thandizo lathu.

Israyeli wolumidwayo atayang'anitsitsa pa njoka ya mkuwa, adalanda dziko la Aamori (vs. 24 & 25) nagonjetsanso dziko la Basana (v. 35)

Kulumwa si mathero a nkhani, okondedwa! Yehova atha kutimenyera ife nkhondo zathu posakumbukira machimo omwe tavomereza ndi kuwasiya. Iye adzatipatsa chigonjetso tikapenyetsetsa pa Yesu.

Okondedwa, tiferenji chisomo chiripo? "Yang'ana pa mtanda kwa Yesuyo, kuti upeze moyowo... 🎶🎵

28/08/2025

Lets vote for Dr Dalitso Kabambe
Ndi UTM party

Pa 16 September pano

Address

Lilongwe Malawi
Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UTM Tv Channel posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share