28/09/2024
Amene muli ku Mzuzu
muthalika mu mzinda wa Mzuzu komwe chipani cha DPP chikuchititsa msonkhano.
Apa mtsogoleri wa chipanichi a Peter Muthalika akufika ku bwalo la Katoto komwe achititse msonkhano wao oyamba patapita nthawi yaitali.
Pangani follow ngati ndinu fans wa DPP