Patriotic Citizens Party - PCP

Patriotic Citizens Party - PCP We are Patriotic. We are Action. We are results. Tikonze Malawi Limodzi

The VP right Honorable Timothy Kaendera interacting with People.P*P Tikonze Malawi Limodzi.Jordan Sauti Tsogolo la Malaw...
12/08/2025

The VP right Honorable Timothy Kaendera interacting with People.

P*P Tikonze Malawi Limodzi.
Jordan Sauti Tsogolo la Malawi
Jordan Sauti Yeee!!

Kutumikira chipani chotsogola komanso  chokondeka cha P*P.Motsogozedwa ndi wachiwiri kwam'tsogoleri wachipanichi Honorab...
08/08/2025

Kutumikira chipani chotsogola komanso chokondeka cha P*P.

Motsogozedwa ndi wachiwiri kwam'tsogoleri wachipanichi Honorable Timothy Kaendera.

P*P Tikonze Malawi Limodzi
Jordan Sauti Tsogolo la Malawi.
Jordan Sauti 16 September YEEE!!

Ife a Chipani cha P*P omwe  tili ndichidwi chofuna kuphula dziko lino pamoto, ndife khumudwa ndimomwe mabungwe ena omwe ...
08/08/2025

Ife a Chipani cha P*P omwe tili ndichidwi chofuna kuphula dziko lino pamoto, ndife khumudwa ndimomwe mabungwe ena omwe siaboma akuchitira.

Munthawi ino yomwe zipani zosiyanasiyana zikukopa anthu kuti adzazivotere pa zisankho zapatatu zomwe zichitike m'dziko muno pa 16 Seputembala chaka chino, mabungwe omwe siabomawa akumasankha zipani zoti akumane nazo kuti azifunse momwe zikuganizilira pamomwe zingatukulire dziko lino, m'magawo osiyanasiyana monga aza; Umoyo, Ulimi, Maphunziro, Zachuma ndi ena ambiri.

Ife a P*P ndiwokhudzidwa ndikusalidwaku, chifukwa ifenso ngati chipani china chilichose cholembetsedwa m'dziko muno tili ndi ufulu ofotokoza zamomwe tidzatukulire dziko lino tikatenga boma pa 16 Seputembala pano.

Lero la Mulungu pa 03 August 2025, Mkulu Oona zakafukufuku komanso kapezedwe kazinthu zosiyanasiyana, ku Chipani Cha Pat...
03/08/2025

Lero la Mulungu pa 03 August 2025, Mkulu Oona zakafukufuku komanso kapezedwe kazinthu zosiyanasiyana, ku Chipani Cha Patriotic Citizens ( P*P), Abusa a Andack Bizwick Robert komanso wapam'pando wa Chipanichi kum'mwera kwadziko lino bambo Laston Grevulo, adakumana ndi akulu akulu ena achipani Cha P*P, ku bangwe pa Sukulu ya Pulayimare ya Masala, munzinda wa Blantyre.

Cholinga cham'kumanowu chidali chofuna kulimbikitsana wina ndinzake pazakumanga chipani chokondedwa Cha P*P.

Mikumano yotereyi ndiyomwe imathandizira kupititsa patsogolo chipani Cha P*P.

Inu Chipani ndichomwechi cha P*P!
Inu M'tsogoleri ndiyemweyu Jordan Sautiyu!

P*P Tikonze Malawi Limodzi!
Jordan Sauti Tsogolo la Malawi!
Jordan Sauti 16 September Yee!

Today at 3:00 PM, the President of the Patriotic Citizens Party (P*P),  Jordan Sauti, will be featured in an Interview c...
03/08/2025

Today at 3:00 PM, the President of the Patriotic Citizens Party (P*P), Jordan Sauti, will be featured in an Interview called The Candidate with Suzgo Chitete of Nation Publications Limited (NPL). This important engagement will be broadcast on Nation Online, offering the public a valuable opportunity to hear directly from one of Malawi’s key political figures.

During the interview, President Sauti is expected to shed light on a range of pressing national issues and share his party’s vision for the country’s development. The discussion will focus on Mining and will also emphacise strategies for economic growth, social progress, governance, and other critical areas impacting the lives of Malawian citizens.

This is a timely and important conversation for all those who care about the future of Malawi. As such, we encourage everyone to tune in to National Online at 3:00 PM today to stay informed and engaged.

Your voice matters. Your awareness is power. Let’s tune in and be part of the national dialogue.

P*P Tikonze Malawi Limodzi
Jordan Sauti Tsogolo la Malawi
Jordan Sauti Yee!!

PRESIDENT JORDAN SAUTI OF PATRIOTIC CITIZENS PARTY(P*P) NAMES HONORABLE  TIMOTHY KAYENDERA AS HIS RUNNING MATE IN 2025 G...
01/08/2025

PRESIDENT JORDAN SAUTI OF PATRIOTIC CITIZENS PARTY(P*P) NAMES HONORABLE TIMOTHY KAYENDERA AS HIS RUNNING MATE IN 2025 GENERAL ELECTIONS AND VICE PRESIDENT OF P*P.

As the nation prepares for the highly anticipated 2025 General Elections scheduled for 16th September 2025, President Jordan Sauti, presidential candidate for the Patriotic Citizens Party (P*P), has officially appointed Honorable Timothy Kayendera as his running mate. The announcement was made on 29th July 2025, during the official submission of nomination papers to the Malawi Electoral Commission (MEC).

This strategic appointment underscores President Sauti’s commitment to forming a strong and experienced leadership team that reflects integrity, competence, and a vision for national progress. Honorable Kayendera, widely respected across the political and financial spheres, brings an extensive background in finance, governance, and leadership, positioning him as a valuable asset in the P*P's campaign and, ultimately, in government.

President Sauti, in his statement during the nomination ceremony, emphasized:

“The decision to appoint Honorable Timothy Kayendera is both symbolic and strategic. His extensive experience in managing financial systems, his dedication to ethical leadership, and his unwavering patriotism make him the right partner in our mission to lead this nation into a prosperous future.”

Honorable Kayendera has served in various high-level public service roles. His career has been marked by a consistent focus on economic reform, fiscal discipline, and inclusive development, earning him both public trust and professional acclaim.

In accepting the nomination, Honorable Kayendera expressed his gratitude and readiness:

“I am deeply honored by the trust placed in me by President Sauti and the Patriotic Citizens Party. This is not just a political appointment—it is a call to national service. I pledge to work tirelessly alongside President Sauti to build a Malawi that is economically resilient, socially just, and democratically strong.”

The Patriotic Citizens Party(P*P) envisions a leadership that prioritizes transparency, empowerment of citizens, economic revitalization, and responsive governance. The Sauti–Kayendera ticket embodies these principles and offers a renewed hope for Malawians seeking pragmatic and people-centered leadership.

As campaign activities continue across the country, the Patriotic Citizens Party invites all citizens to engage with its vision and take part in shaping a brighter, unified future.

P*P Tikonze Malawi Limodzi
Jordan Sauti Tsogolo la Malawi.
Jordan Sauti 16 September Yeee!!

Department of Communications and Marketing
Patriotic Citizens Party(P*P).

The Citizens Patriotic Party (P*P) would like to extend its deepest and most sincere gratitude to all the patriotic Mala...
29/07/2025

The Citizens Patriotic Party (P*P) would like to extend its deepest and most sincere gratitude to all the patriotic Malawians who came out in large numbers today, to show unwavering support during a historic moment in our party’s journey, the submission of presidential nomination papers by our President and torchbearer, Jordan Sauti, to the Malawi Electoral Commission (MEC).

This significant event, held at the Bingu International Convention Centre (BICC) in Lilongwe, marks a pivotal step in our collective pursuit of a better, united, and prosperous Malawi. Your presence, enthusiasm, discipline, and unity demonstrated the true spirit of the Citizens Patriotic Party and reaffirmed that this movement belongs to the people.

We were moved by the passion, energy, and hope reflected on every face, and we acknowledge all those who traveled from near and far, across towns, villages, and districts, to witness this important milestone. Your participation not only energized our President and leadership but also sent a clear message: Malawians are ready for a new kind of leadership rooted in integrity, accountability, and service.

We also extend our thanks to the Malawi Electoral Commission for facilitating a smooth and professional nomination process, and to the security personnel who ensured the safety and order of all attendees.

As we move forward in this election season, we call upon all citizens to remain peaceful, informed, and engaged. The future of our nation lies in our hands, and together, through unity and collective action, we shall build the Malawi we all deserve.

Once again, thank you for standing with us. Let us continue to walk together with courage, dignity, and purpose.

P*P Tikonze Malawi Limodzi
Jordan Sauti Yeee

It's TODAYSubmission of Nomination Papers @  MEC by the Incoming 7th President of Republic of Malawi JORDAN SAUTI P*P Ti...
29/07/2025

It's TODAY

Submission of Nomination Papers @ MEC by the Incoming 7th President of Republic of Malawi JORDAN SAUTI

P*P Tikonze Malawi Limodzi.
Jordan Sauti Yeee!

JORDAN SAUTI, the incoming 7th President of the Republic of Malawi, will submit his Nomination Papers tommorrow, Tuesday...
28/07/2025

JORDAN SAUTI, the incoming 7th President of the Republic of Malawi, will submit his Nomination Papers tommorrow, Tuesday, 29 July 2025, @ BICC, Lilongwe.

Please join us.
P*P - Change Malawi has been waiting for.

P*P - Tikonze Malawi Limodzi.
Jordan Sauti Yeee!

ANZANGA!! MALAWI NTHAWI YAKWANA.1)  Nthawi yakwana: Malawi ayambe kukhala dziko lozidalira pa chuma.3) Nthawi yakwana: M...
26/07/2025

ANZANGA!! MALAWI NTHAWI YAKWANA.

1) Nthawi yakwana: Malawi ayambe kukhala dziko lozidalira pa chuma.

3) Nthawi yakwana: Malawi awonetse kuthekera kwa nzika zake.

4) Nthawi yakwana: Kuti nzika za Malawi zitukuke koposa.

5) Nthawi yakwana: Malawi alamulidwa ndi Jordan Sauti.

Kodi mukuziwa kuti m’maboma 20 pa 28 amuMalawi muno muli golide ochuluka?

P*P – Tikonze Malawi Limodzi.
VOTERANI JORDAN SAUTI.

MALAWI IMVA IZI:M'tsogoleri oyamba ku Malawi opanda banga linalirilonse. Uyu ndiye chiyembekezo cha Malawi. Uyu ndi Jord...
25/07/2025

MALAWI IMVA IZI:

M'tsogoleri oyamba ku Malawi opanda banga linalirilonse. Uyu ndiye chiyembekezo cha Malawi. Uyu ndi Jordan Sauti.

Katswiri pankhani zowonetsetsa kuti chumadi chikuchokera mnthaka, inde uyu ndikatakwe pankhani zamigodi, ndikatsirinso pa za technology. Mayiko ambiri akupindula ndi ukadaulo a Sauti.
Pulezidenti Jordan Sauti wachiwonanso cham'tengo wapatari kuti atumikire Malawi kwathunthu ngati M'tsogoleri kuyambira pa 16 Seputembala pano.
Azindikiritse Malawi kuti mnthakamu muli chuma chadzawoneni, muli miyala yomwe ili ndikuthekera kubweretsa chuma chokonzeranso Malawi.

Anthu onse vomerezani kuti M'tsogoleri ndi Jordan Sauti basi.

P*P – Tikonze Malawi Limodzi.
Jordan Sauti Yeee!!

24/07/2025

P*P yakonzeka kusintha Malawi kwathunthu.
Pa 16 Seputembala pano Mulungu,Chisumphi,Namalenga wasankha kale P*P kuti ikonze dzikoli.

P*P, Tikonze Malawi Limodzi.
Jordan Sauti, YEEEE

Address

Akulenje Building
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Patriotic Citizens Party - PCP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share