Tijede MU NDALE

Tijede MU NDALE Taking part in the running of government affairs

12/06/2024

Mudyereni nsima afitiinu👺👹

05/08/2022

OCHIRIMA MUTIPO?NDE MWADEKHATU DALA😂😂

28/07/2022

Nayeso Namiwayo asakhaletu atamenya ija Moses Kumkuyu komaso ija ya Kamulepoism😂😂
Ndawala patauni🏃🏃

14/07/2022

Afana oganiza boh! Where is the issue of harmonization of salaries for civil servants?

01/07/2022

Apapa ndipamene mungaziweno kuti Chilima ndi UTM anabwera kuzakhala,mfana oganiza boh kuzangoipatsa moto🔥🔥

23/06/2022

Bus ndiyomweyo mmalomokwera anthu akukwera ndimafuta,atipha.

22/06/2022

Komatu tiyembekezere fire mabomba kuchokera kwa Chilima,80+ names enawa akuwabisa chifukwa cha?🤔🤔

17/06/2022

Apumbwa aja🐦🐦 ndi achulewa🐸🐸 bola ndani?

10/06/2022

Munyengo ya achuleyi akuti chani kwanuko za Malawi the frogs?

03/06/2022

Zandale tiike kae apo koma Gwamba uja anabwera kuzakhala akukwanila pa u landlord✊✊

02/06/2022

Bwampini bon kalingonda watitu ziiii ngati za devaluation ya kwacha sanamve😂😂😂

01/06/2022

Ifetimayesa akufuna kulengeza kwa ntundu wa amalawi kuti bomalandikanika basi ndikutula udindo pansi🤔🤔🤔

Address

Ndirande Makata
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tijede MU NDALE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share