Department of Climate Change and Meteorological Services

Department of Climate Change and Meteorological Services The Official page of the Department of Climate Change & Meteorological Services .

Updates on Weather, Climate, Alerts & News for informed decisions https://bit.ly/m/dccms

06/09/2026

06/09/2026
Zanyengo Madzulo ndi Alex

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 07 SEPTEMBER 2026 Tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali, yofunda n...
06/09/2026

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 07 SEPTEMBER 2026

Tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali, yofunda ndi ya changululu usiku uno ndi mawa m’mawa.

Mawa masana, tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali, mphepo, yotentha ndi yachangululu.

Chenjezo: Mphepo ya mwera iyamba kuomba pa nyanja ya Malawi ndi nyanja zina kuyambira mawa madzulo. Onse ogwiritsa ntchito nyanjazi akulangizidwa kukhala atcheru tuti titeteze miyoyo ndi katundu.

MPHEPO: Iziomba kuchokera kum’mwera chakumvuma...
LACHIWIRI: Nyengo ya mitambo yapatalipatali ndi yotentha…

Mukafuna kudziwa nyengo ya dera lanu pangani dowunilodi apu ya zanyengo (zanyengo app) pa foni yanu ya m'manja yomwe mungaipeze pa gugo puleyi sitoro (google play store) pogwiritsa ntchito link iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.zanyengo&pli=1

06/09/2026

06/09/2026
Zanyengo M'mawa ndi Alex

05/09/2026

05/09/2026
Zanyengo Madzulo ndi Alex

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 6TH SEPTEMBER 2026Tiyembekezere nyengo yozizira pan’gono ndi yopanda mitamb...
05/09/2026

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 6TH SEPTEMBER 2026
Tiyembekezere nyengo yozizira pan’gono ndi yopanda mitambo usiku uno komanso yachangululu mawa m’mawa.

Mawa masana, tiyembekezere nyengo yamphepo, yadzuwa, yotentha ndi yachangululu.

MPHEPO: Iziomba kuchokera chakumvuma...
LOLEMBA: Nyengo ya mitambo yapatalipatali ndi ya mphepo…

Mukafuna kudziwa nyengo ya dera lanu pangani dowunilodi apu ya zanyengo (zanyengo app) pa foni yanu ya m'manja yomwe mungaipeze pa gugo puleyi sitoro (google play store) pogwiritsa ntchito link iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.zanyengo&pli=1

05/09/2026

Morning weather bulletin on 5 September 2026 with Noel

05/09/2026

Salomy ndi admin a weekend akupatsirani zanyengo za lero pa 5 Septermber 2026. Zigubu za madzi m'manja pamene nyengo yotentha ikupitilira

04/09/2026

Zanyengo madzulo pa 4 September 2026 ndi Salomy Banda

04/09/2026

Evening weather broadcast issued 4 September 2026 with Noel

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 05 SEPTEMBER 2026Tiyembekezere nyengo yozizira pan’gono ndi ya mitambo yapa...
04/09/2026

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 05 SEPTEMBER 2026
Tiyembekezere nyengo yozizira pan’gono ndi ya mitambo yapatalipatali usiku uno komanso yachangululu mawa m’mawa.

Mawa masana, tiyembekezere nyengo yamphepo, yadzuwa, yotentha ndi yachangululu.

MPHEPO: Iziomba kuchokera chakumvuma...

LOWERUKA: Nyengo ya mitambo yapatalipatali ndi yotentha…

Address

Victoria Avenue
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Department of Climate Change and Meteorological Services posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Department of Climate Change and Meteorological Services:

Shortcuts

Share