The Tobacco Commission

The Tobacco Commission We regulate the to***co industry in Malawi, promoting the production and marketing of the country's green gold.

Tikudziwitsa alimi onse amene anagulitsa fodya wopitirira mulingo umene alimiwo anapatsidwa kuti ndalama za fodya ameney...
18/08/2026

Tikudziwitsa alimi onse amene anagulitsa fodya wopitirira mulingo umene alimiwo anapatsidwa kuti ndalama za fodya ameneyu ziri ndi ife.

Alimi amene anagulitsa fodya ameneyu pasanadutse pa 14 August chaka chino alandira ndalama zawo pofika lachisanu pa 28 August.

Tikutsimikizira alimi onse okhudzidwa kuti alandira ndalama zawo mwachangu.

Ministry of Agriculture - Malawi TAMA Farmers Trust NASFAM

Lero madzulo ano tikhala tiri pa wayilesi ya Zodiak kufotokoza za KYG.Programme imeneyi iyamba 5 koloko.Pakhalanso mwayi...
10/08/2026

Lero madzulo ano tikhala tiri pa wayilesi ya Zodiak kufotokoza za KYG.

Programme imeneyi iyamba 5 koloko.

Pakhalanso mwayi woyimba ma phone kufunsa mafunso okhudza KYG.

Tiyeni tikhalire limodzi.

01/08/2026

Sabata imodzi yatha chiyambireni KYG. Amzanu achita kale. Inu muchita liti?

TAMA Farmers Trust NASFAM Agricultural Research and Extension Trust - ARET Ministry of Agriculture - Malawi

Tikuti titsindike kuti pobwera kudzachita KYG komanso kudzakhomera, ma membala ONSE pa kalabu akuyenera kubwera. Kaya pa...
27/07/2026

Tikuti titsindike kuti pobwera kudzachita KYG komanso kudzakhomera, ma membala ONSE pa kalabu akuyenera kubwera.

Kaya pa kalabu pali ma membala 5 kaya angati, onsewo abwere kuti zitheke.

Kukhomera zitupa tikuyamba lolemba pa 27 July. Kukhomera ndi pafupifupi K24.00 pa kg.

Pa tsiku lomwelo la 27 July, tikhalanso tikuyamba ntchito yodziwa alimi onse mu ndondomeko imene tikuyitchula KYG (Know Your Grower).

Mlimi aliyense akuyenera alembetse mu kalondolondo wa KYG kuti adzathe kugulitsa fodya wake chaka cha mawa.

Tikhala tikufotokoza zambiri za ndondomeko ya KYG pompano komanso mma wayilesi ndi kanema.

Zambiri ziri mu kalata iyi:

Ministry of Agriculture - Malawi TAMA Farmers Trust NASFAM Agricultural Research and Extension Trust - ARET

22/07/2026

Nkhani ya Know Your Grower (KYG) ija tikufotokozera motere pang'ono:

Kukhomera zitupa tikuyamba lolemba pa 27 July. Kukhomera ndi pafupifupi K24.00 pa kg.Pa tsiku lomwelo la 27 July, tikhal...
22/07/2026

Kukhomera zitupa tikuyamba lolemba pa 27 July. Kukhomera ndi pafupifupi K24.00 pa kg.

Pa tsiku lomwelo la 27 July, tikhalanso tikuyamba ntchito yodziwa alimi onse mu ndondomeko imene tikuyitchula KYG (Know Your Grower).

Mlimi aliyense akuyenera alembetse mu kalondolondo wa KYG kuti adzathe kugulitsa fodya wake chaka cha mawa.

Tikhala tikufotokoza zambiri za ndondomeko ya KYG pompano komanso mma wayilesi ndi kanema.

Zambiri ziri mu kalata iyi:

Ministry of Agriculture - Malawi TAMA Farmers Trust NASFAM Agricultural Research and Extension Trust - ARET

Zochitika pa ulimi wa fodya komanso ku msika ndi zambiri. Inu alimi, musamaphonyane nazo. Chitani follow Whatsapp channe...
17/07/2026

Zochitika pa ulimi wa fodya komanso ku msika ndi zambiri. Inu alimi, musamaphonyane nazo. Chitani follow Whatsapp channel yatgu pochita click link iyi
https://whatsapp.com/channel/0029VbD4sb35q08YrnyLoJ16 kuti mudzitsatira bwino mmene zinthu ziliri.

Ministry of Agriculture - Malawi TAMA Farmers Trust NASFAM

Follow To***co Commission - Alimi's WhatsApp channel. Kudziwitsa alimi za ulimi ndi malonda a fodya m'Malawi. Join 560 followers for the latest updates.

09/07/2026
Excited to see that the Know Your Grower (KYG) project we will  embark on this year is gaining strong backing from the c...
30/06/2026

Excited to see that the Know Your Grower (KYG) project we will embark on this year is gaining strong backing from the country’s to***co buying companies. They say the initiative is long overdue.

With KYG, we will ensure 100% of Malawi's to***co is fully traceable before the 2027 marketing season.

That’s a major milestone for the future of our green gold!

Since last week, our team has been presenting the KYG concept to the companies to ensure they understand the design and to gather their valuable input. We have already engaged 6 of the current 8 buying companies. We will soon meet all of them, alongside grower associations TAMA Farmers TrustNASFAM, our partners at Agricultural Research and Extension Trust - ARET and Ministry of Agriculture - Malawi

Why this project is so important:

✅Enhanced Traceability: We will be able to trace all the to***co to its source.

✅ ESG Compliance: Will promote strict compliance with Environmental, Social, and Governance (ESG) standards across the value chain.

✅ Industry Sustainability: Will strengthen international confidence in the integrity of Malawi's to***co.

We need your support. Let’s work together to build a more sustainable and globally competitive to***co industry.

Address

Kanengo
Lilongwe
265

Opening Hours

Monday 07:30 - 16:30
Tuesday 07:30 - 16:30
Wednesday 07:30 - 16:30
Thursday 07:30 - 16:30
Friday 07:30 - 16:30

Telephone

+265998256545

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Tobacco Commission posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to The Tobacco Commission:

Shortcuts

Share