Bolani Chakwera

Bolani Chakwera Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bolani Chakwera, Political organisation, Mzimba Street, Lilongwe.

31/05/2026
Lamulungu lopambanaKhalani M'modzi wa Ife Powuza Wina ndi Ena30 June, 2026 Tikavote Mwa UnyinjiInde Tumeni Ndavomera Ndi...
31/05/2026

Lamulungu lopambana

Khalani M'modzi wa Ife Powuza Wina ndi Ena
30 June, 2026 Tikavote Mwa Unyinji
Inde Tumeni Ndavomera Ndikayimilire Inuyo

Ulendo Uno Tipose 8200 Votes Ija
Komaso Tinagwilizana Kale

Join my campaign today........



Ayikatu mtsonkho pa Panadol, Bufen, Amoxicillin ndi mamkhwala ena amene  timagwilitsa ntchito tsiku ndi tsiku. Economy y...
30/05/2026

Ayikatu mtsonkho pa Panadol, Bufen, Amoxicillin ndi mamkhwala ena amene timagwilitsa ntchito tsiku ndi tsiku. Economy ya Mwanamveka mukuiwona bwanji akuluakulu, atithandiza uyuyu koma?.

10 pa 10 Dr Laz, 💪Akamuna!!!!!
30/05/2026

10 pa 10 Dr Laz, 💪

Akamuna!!!!!

LAGWA LOKHA BOMA LIJA KUNO!Nde ena nkumati we are on the right track economically? 🤣🤣🤣🤣🤣
30/05/2026

LAGWA LOKHA BOMA LIJA KUNO!

Nde ena nkumati we are on the right track economically?

🤣🤣🤣🤣🤣

Nde pali uchitsilu wina pa FB pano, Makhadethi sakumafuna kuti ulembe zoyipa za DPP ndi APM, ati tonse tizingowombela mm...
30/05/2026

Nde pali uchitsilu wina pa FB pano, Makhadethi sakumafuna kuti ulembe zoyipa za DPP ndi APM, ati tonse tizingowombela mmanja basi.FB yasandukanso ya Mulhakho? 🤣🤣🤣🤣

 PRESIDENT CHAKWERA TO ATTEND FUNERAL IN NKHATABAYHis Excellency Dr Lazarus Chakwera , the 6th President of the Republic...
30/05/2026



PRESIDENT CHAKWERA TO ATTEND FUNERAL IN NKHATABAY

His Excellency Dr Lazarus Chakwera , the 6th President of the Republic of Malawi and President of the Malawi Congress Party (MCP), accompanied by the former First Lady, Madame Monica Chakwera , will today, Saturday, May 30th, 2026, attend the funeral of the late nephew of the former First Lady, Madame Monica Chakwera, in Nkhatabay District.

In accordance with our tradition, all those residing in Nkhatabay and surrounding areas are warmly invited and encouraged to join His Excellency in large numbers as he pays his final respects to the deceased. Your presence will provide comfort and support during this time around.

Address

Mzimba Street
Lilongwe
AREA10

Telephone

+265999138043

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bolani Chakwera posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Bolani Chakwera:

Share