DPP

DPP Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DPP, Political Party, Lilongwe area 46, Lilongwe.

28/08/2026

  .Awa ndi Ma artist omwetikuyenera kumawaitana kuzaimba kwathukuno sizachina luga zanuzija. munthu tampasa dollar zambi...
28/08/2026

.

Awa ndi Ma artist omwetikuyenera kumawaitana kuzaimba kwathukuno sizachina luga zanuzija. munthu tampasa dollar zambirimbiri nkumatitengaso ngati mazoba. artistasamazinve ...

 YESU atangofika nyumba yopemphereramo anasokoneza ma bussines awanthu , ndikuyamba kulalikiramo uthenga wa chirungamo.....
28/08/2026



YESU atangofika nyumba yopemphereramo anasokoneza ma bussines awanthu , ndikuyamba kulalikiramo uthenga wa chirungamo.. atangotero eeeee afalitsi, asaduki, mavenda anayamba kumuda coz zinthu zawo zinasiya kuyenda, umangonva bola chakwera yemweuja. ati ndalama imaoneka kuzolowera ziphuphu ndikuba basi.

Ati analandira messege ya NTUKULA PAKHOMO.
25/08/2026

Ati analandira messege ya NTUKULA PAKHOMO.

Mumatinena ife tikabesa dollar pa airtel money...... Amalawi sitinasukusulebe.
25/08/2026

Mumatinena ife tikabesa dollar pa airtel money...... Amalawi sitinasukusulebe.

vuto mumachedwa ndikutembelera anzanu osaziwa zabwino zomwe Mulungu wamukonzera nzanuyo.
22/08/2026

vuto mumachedwa ndikutembelera anzanu
osaziwa zabwino zomwe Mulungu wamukonzera nzanuyo.

21/08/2026

(JB)

Munthu wankulu
19/08/2026

Munthu wankulu

 Kususa ndikuonera mpira komwe.ndale zakumalawi
17/08/2026


Kususa ndikuonera mpira komwe.
ndale zakumalawi

  KOMABE ASIKANAWA AYESESABE OSATI NTCHEMBERE ZACHIMUNA TILINAZO KUNOZI
17/08/2026


KOMABE ASIKANAWA AYESESABE OSATI NTCHEMBERE ZACHIMUNA TILINAZO KUNOZI

Address

Lilongwe Area 46
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DPP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share